14 Choncho Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndiponso anthu ena onse. Ndipo iwo anabwera nʼkuyamba kugwira ntchito panyumba ya Mulungu wawo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+