Nehemiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.
2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.