4 Ezara wokopera Malembayo, anaima pansanja yamatabwa imene anaimanga chifukwa cha mwambowu. Kumanja kwake kunaima Matitiya, Sema, Anaya, Uriya, Hilikiya ndi Maaseya. Kumanzere kwake kunali Pedaya, Misayeli, Malikiya,+ Hasumu, Hasi-badana, Zekariya ndi Mesulamu.