-
Ezara 8:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Popeza dzanja labwino la Mulungu wathu linkatithandiza, iwo anatibweretsera munthu wanzeru wochokera pakati pa ana a Mali+ mdzukulu wa Levi mwana wa Isiraeli. Dzina lake linali Serebiya+ ndipo anabwera limodzi ndi ana ake komanso abale ake. Onse pamodzi analipo 18. 19 Panalinso Hasabiya, yemwe anali pamodzi ndi Yesaiya wochokera pa ana a Merari,+ abale ake ndi ana awo. Onse pamodzi analipo 20.
-