Ezara 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa ana a Pahati-mowabu+ panali Adena, Kelali, Benaya, Maaseya, Mataniya, Bezaleli, Binui ndi Manase. Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anatenga akazi achilendo+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.+ Nehemiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malikiya mwana wa Harimu+ komanso Hasubu mwana wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo ndi Nsanja ya Mauvuni.+
30 Pa ana a Pahati-mowabu+ panali Adena, Kelali, Benaya, Maaseya, Mataniya, Bezaleli, Binui ndi Manase.
11 Malikiya mwana wa Harimu+ komanso Hasubu mwana wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo ndi Nsanja ya Mauvuni.+