Ezara 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+ Ezara 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Zatu,+ 945. Ezara 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa ana a Zatu+ panali Elioenai, Eliyasibu, Mataniya, Yeremoti, Zabadi ndi Aziza. Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anatenga akazi achilendo+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.+
2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+