2 Choncho iye anapita kukakumana ndi Asa nʼkumuuza kuti: “Tamverani mfumu Asa ndi anthu onse a fuko la Yuda ndi Benjamini. Yehova akhala nanu inuyo mukapitiriza kukhala naye.+ Mukamufunafuna iye adzalola kuti mumʼpeze,+ koma mukamusiya nayenso adzakusiyani.+