-
Nehemiya 6:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia, Gesemu Muluya+ komanso adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo ndatseka mipata yonse (ngakhale kuti pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko mʼmageti),+ 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.
-