Nehemiya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera pamenepo, ndinagwira nawo ntchito yomanga mpandawo ndipo sitinakhale ndi minda.+ Atumiki anga onse anasonkhana kumeneko kuti agwire ntchito.
16 Kuwonjezera pamenepo, ndinagwira nawo ntchito yomanga mpandawo ndipo sitinakhale ndi minda.+ Atumiki anga onse anasonkhana kumeneko kuti agwire ntchito.