Nehemiya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a anthuwo ankakhala ku Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi pa anthu 10 alionse woti akakhale ku Yerusalemu, mzinda woyera, ndipo anthu 9 otsalawo ankakhala mʼmizinda ina.
11 Akalonga a anthuwo ankakhala ku Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi pa anthu 10 alionse woti akakhale ku Yerusalemu, mzinda woyera, ndipo anthu 9 otsalawo ankakhala mʼmizinda ina.