Ekisodo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Ndikugwetserani chakudya kuchokera kumwamba ngati mvula,+ ndipo aliyense azitola muyezo womukwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese kuti ndione ngati angatsatire chilamulo changa kapena ayi.+
4 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Ndikugwetserani chakudya kuchokera kumwamba ngati mvula,+ ndipo aliyense azitola muyezo womukwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese kuti ndione ngati angatsatire chilamulo changa kapena ayi.+