-
Ekisodo 16:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mame aja atauma, panthaka yamʼchipululumo panapezeka tinthu topyapyala ndi tolimba koma tosalala+ ngati madzi amene aundana panthaka. 15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+
-