Nehemiya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinaika Haneni mʼbale wanga+ ndi Hananiya, mkulu wa mʼNyumba ya Chitetezo Champhamvu,+ kuti aziyangʼanira Yerusalemu. Hananiya anali munthu wodalirika ndiponso woopa Mulungu woona+ kuposa anthu ena ambiri.
2 Kenako ndinaika Haneni mʼbale wanga+ ndi Hananiya, mkulu wa mʼNyumba ya Chitetezo Champhamvu,+ kuti aziyangʼanira Yerusalemu. Hananiya anali munthu wodalirika ndiponso woopa Mulungu woona+ kuposa anthu ena ambiri.