Numeri 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pambuyo pake, anatembenuka nʼkulowera Njira ya ku Basana. Ndiyeno Ogi+ mfumu ya ku Basana anabwera limodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nawo ku Edirei.+ Numeri 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti palibe ndi mmodzi yemwe amene anapulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+
33 Pambuyo pake, anatembenuka nʼkulowera Njira ya ku Basana. Ndiyeno Ogi+ mfumu ya ku Basana anabwera limodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nawo ku Edirei.+
35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti palibe ndi mmodzi yemwe amene anapulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+