4 Ndinapemphera kwa Yehova Mulungu wanga nʼkuvomereza machimo athu kuti:
“Inu Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu komanso wochititsa mantha. Inu mumakwaniritsa pangano lanu ndipo mumasonyeza chikondi chokhulupirika+ kwa anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu.+