Ezara 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Yesuwa, ana ake ndi abale ake, Kadimiyeli ndi ana ake, ndi ana a Yuda,* ananyamuka mogwirizana kuti akayangʼanire anthu ogwira ntchito mʼnyumba ya Mulungu woona. Panalinso ana a Henadadi,+ ana awo ndi abale awo, omwe anali Alevi. Nehemiya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa, Binui, Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndiponso Mataniya,+ amene ankatsogolera nyimbo zotamanda Mulungu limodzi ndi abale ake.
9 Choncho Yesuwa, ana ake ndi abale ake, Kadimiyeli ndi ana ake, ndi ana a Yuda,* ananyamuka mogwirizana kuti akayangʼanire anthu ogwira ntchito mʼnyumba ya Mulungu woona. Panalinso ana a Henadadi,+ ana awo ndi abale awo, omwe anali Alevi.
8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa, Binui, Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndiponso Mataniya,+ amene ankatsogolera nyimbo zotamanda Mulungu limodzi ndi abale ake.