-
Nehemiya 13:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndinazindikiranso kuti Alevi sankapatsidwa magawo awo, moti Alevi+ ndiponso oimba amene ankatumikira anachoka,+ ndipo aliyense anapita kumunda wake.+ 11 Choncho ndinadzudzula atsogoleriwo+ ndipo ndinawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani nyumba ya Mulungu woona yasiyidwa chonchi?”+ Kenako ndinawasonkhanitsa nʼkuwabwezera pa ntchito zawo.
-