1 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+ 1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri. Ezara 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+ Ezara 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a alonda apageti:+ ana a Salumu, ana a Ateri, ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita ndi ana a Sobai, onse analipo 139. Nehemiya 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ ankalondera mageti.+ Iwo ankalondera zipinda zosungira zinthu zomwe zinali pafupi ndi mageti.
2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+
17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri.
2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+
42 Ana a alonda apageti:+ ana a Salumu, ana a Ateri, ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita ndi ana a Sobai, onse analipo 139.
25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ ankalondera mageti.+ Iwo ankalondera zipinda zosungira zinthu zomwe zinali pafupi ndi mageti.