Nehemiya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene ndinaikidwa kukhala bwanamkubwa wawo+ mʼdziko la Yuda, kuyambira chaka cha 20+ mpaka chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+
14 Komanso kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene ndinaikidwa kukhala bwanamkubwa wawo+ mʼdziko la Yuda, kuyambira chaka cha 20+ mpaka chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+