-
Nehemiya 10:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Komanso tinachita maere okhudza nkhuni zimene ansembe, Alevi ndi anthu ankayenera kubweretsa kunyumba ya Mulungu wathu, mogwirizana ndi nyumba za makolo athu. Ankayenera kuzibweretsa pa nthawi zoikidwiratu, chaka chilichonse kuti aziziyatsa paguwa lansembe la Yehova Mulungu wathu, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo.+
-