Ezara 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa ana a Bebai+ panali Yehohanani, Hananiya, Zabai ndi Atilai. Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anatenga akazi achilendo+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.+