Esitere 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Esitere sananene zokhudza abale ake ndiponso anthu a mtundu wake,+ mogwirizana ndi zimene Moredikayi anamulangiza. Esitere ankachita zimene Moredikayi wanena ngati mmene ankachitira pa nthawi imene ankakhala naye.+
20 Esitere sananene zokhudza abale ake ndiponso anthu a mtundu wake,+ mogwirizana ndi zimene Moredikayi anamulangiza. Esitere ankachita zimene Moredikayi wanena ngati mmene ankachitira pa nthawi imene ankakhala naye.+