-
Esitere 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ngati mungandikomere mtima mfumu ndiponso ngati mungakonde kundipatsa zimene ndapempha nʼkuchita zomwe ndikufuna, inu mfumu ndi Hamani mubwere kuphwando limene ndidzakukonzereni mawa. Ndipo mawa ndidzakuuzani pempho langa ngati mmene inu mfumu mwanenera.”
-