Genesis 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndidzabweretsa chigumula+ padziko lapansi kuti chiwononge chamoyo chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mpweya wa moyo* mʼthupi lake. Chilichonse chimene chili padziko lapansi chidzawonongedwa.+
17 Ine ndidzabweretsa chigumula+ padziko lapansi kuti chiwononge chamoyo chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mpweya wa moyo* mʼthupi lake. Chilichonse chimene chili padziko lapansi chidzawonongedwa.+