Yobu 4:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iyetu sakhulupirira atumiki ake,Ndipo angelo* ake amawapezera zifukwa. 19 Nanga kuli bwanji anthu amene amakhala mʼnyumba zadothi,Amene maziko awo ali mʼfumbi?+Amene amathudzulidwa mosavuta ngati kadziwotche.
18 Iyetu sakhulupirira atumiki ake,Ndipo angelo* ake amawapezera zifukwa. 19 Nanga kuli bwanji anthu amene amakhala mʼnyumba zadothi,Amene maziko awo ali mʼfumbi?+Amene amathudzulidwa mosavuta ngati kadziwotche.