Yobu 22:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi uyenda panjira yakalekaleImene anthu oipa anayendamo,16 Anthu amene imfa inawatenga nthawi yawo isanakwane,*Amene maziko awo anakokoloka ndi madzi osefukira?*+
15 Kodi uyenda panjira yakalekaleImene anthu oipa anayendamo,16 Anthu amene imfa inawatenga nthawi yawo isanakwane,*Amene maziko awo anakokoloka ndi madzi osefukira?*+