Yobu 15:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi munthu ndi ndani kuti akhale woyera?Kapena aliyense wobadwa kwa mkazi kuti akhale wolungama?+ 15 Iyetu sakhulupirira angelo ake,Ndipo ngakhale kumwamba si koyera mʼmaso mwake.+
14 Kodi munthu ndi ndani kuti akhale woyera?Kapena aliyense wobadwa kwa mkazi kuti akhale wolungama?+ 15 Iyetu sakhulupirira angelo ake,Ndipo ngakhale kumwamba si koyera mʼmaso mwake.+