Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikulu kwambiri inu Yehova!+ Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Mlaliki 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chilichonse iye anachipanga chokongola* ndiponso pa nthawi yake.+ Komanso anapatsa anthu mtima wofuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale. Komabe anthu sadzadziwa ntchito imene Mulungu woona wagwira kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto. Yesaya 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Chifukwa mofanana ndi kumwamba kumene kuli pamwamba kuposa dziko lapansi,Njira zanganso nʼzapamwamba kuposa njira zanuNdipo maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+
11 Chilichonse iye anachipanga chokongola* ndiponso pa nthawi yake.+ Komanso anapatsa anthu mtima wofuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale. Komabe anthu sadzadziwa ntchito imene Mulungu woona wagwira kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto.
9 “Chifukwa mofanana ndi kumwamba kumene kuli pamwamba kuposa dziko lapansi,Njira zanganso nʼzapamwamba kuposa njira zanuNdipo maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+