-
Salimo 18:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndidzathamangitsa adani anga nʼkuwapeza,
Sindidzabwerera mpaka onse nditawawononga.
-
-
Salimo 18:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Iwo amafuula kuti athandizidwe, koma palibe amene angawapulumutse,
Amafika pofuulira Yehova, koma iye samawayankha.
-
-
Yakobo 4:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mukapempha, simulandira chifukwa mumapempha ndi cholinga choipa, kuti mukhutiritse zilakolako za matupi anu.
-