Salimo 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa inuyo Yehova ndi amene mumayatsa nyale yanga,Mulungu wanga amandiunikira mumdima.+ Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,Komanso kuwala kounikira njira yanga.+