Miyambo 6:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Usasirire kukongola kwake mumtima mwako.+Kapena kulola kuti ukopeke ndi maso ake achikoka,26 Munthu amafika potsala ndi mkate umodzi wokha chifukwa cha hule,+Koma mkazi wa mwini amasaka moyo wako wamtengo wapatali. Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+
25 Usasirire kukongola kwake mumtima mwako.+Kapena kulola kuti ukopeke ndi maso ake achikoka,26 Munthu amafika potsala ndi mkate umodzi wokha chifukwa cha hule,+Koma mkazi wa mwini amasaka moyo wako wamtengo wapatali.
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+