-
Genesis 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Pambuyo pake, iwo anamva mawu a Yehova Mulungu pamene iye ankayendayenda mʼmundamo pa nthawi imene kamphepo kayeziyezi kankaomba. Mwamuna ndi mkaziyo atamva, anabisala pakati pa mitengo ya mʼmundamo kuti Yehova Mulungu asawaone.
-
-
Machitidwe 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Petulo anamufunsa kuti: “Tandiuza, kodi ndalama zonse zimene mwapeza mutagulitsa munda wanu ndi izi?” Iye anayankha kuti: “Inde, ndi zomwezo.”
-