1 Mafumu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, anauza Ahabu kuti: “Pitani mukatenge munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, chifukwa Naboti panopa wafa.”
15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, anauza Ahabu kuti: “Pitani mukatenge munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, chifukwa Naboti panopa wafa.”