Mateyu 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino pamene muli oipa? Chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Luka 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino pamene muli oipa? Chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+