Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+ Salimo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thupi langa lonse lachita dzanzi ndipo ndilibiretu mphamvu.Ndikubuula mokweza* chifukwa cha kuvutika kwa mtima wanga.
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+
8 Thupi langa lonse lachita dzanzi ndipo ndilibiretu mphamvu.Ndikubuula mokweza* chifukwa cha kuvutika kwa mtima wanga.