Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera kwambiri.+ Kenako Aroni atatembenuka nʼkumuyangʼana Miriamu, anaona kuti wachita khate.+
10 Mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera kwambiri.+ Kenako Aroni atatembenuka nʼkumuyangʼana Miriamu, anaona kuti wachita khate.+