Yobu 7:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+ 7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zinthu zosangalatsa.* Salimo 103:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu.+Iye amaphuka ngati duwa lakutchire.+ 16 Koma mphepo ikawomba limafa,Ndipo zimangokhala ngati panalibepo.*
6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+ 7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zinthu zosangalatsa.*
15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu.+Iye amaphuka ngati duwa lakutchire.+ 16 Koma mphepo ikawomba limafa,Ndipo zimangokhala ngati panalibepo.*