Genesis 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mulungu anapatsa kuwalako dzina lakuti Masana, koma mdimawo anaupatsa dzina lakuti Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali mʼmawa, tsiku loyamba. Salimo 74:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Masana ndi anu, usikunso ndi wanu. Munapanga kuwala* komanso dzuwa.+
5 Ndiyeno Mulungu anapatsa kuwalako dzina lakuti Masana, koma mdimawo anaupatsa dzina lakuti Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali mʼmawa, tsiku loyamba.