Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamalamulira, nthawi zonse mumachita zinthu mwachilungamo komanso molungama.+Nthawi zonse mumasonyeza kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo.
14 Mukamalamulira, nthawi zonse mumachita zinthu mwachilungamo komanso molungama.+Nthawi zonse mumasonyeza kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika.+
23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo.