Yesaya 38:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikungokhalira kulira ngati namzeze kapena kamwana ka mbalame.+Ndikungokhalira kubuula ngati njiwa.+ Ndatopa ndi kudikirira thandizo kuchokera kumwamba.+ Choncho ndinati: ‘Inu Yehova ine ndapanikizika kwambiri.Chonde ndithandizeni.’+
14 Ndikungokhalira kulira ngati namzeze kapena kamwana ka mbalame.+Ndikungokhalira kubuula ngati njiwa.+ Ndatopa ndi kudikirira thandizo kuchokera kumwamba.+ Choncho ndinati: ‘Inu Yehova ine ndapanikizika kwambiri.Chonde ndithandizeni.’+