Salimo 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, chikondi chanu chokhulupirika chafika kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika mpaka mʼmitambo. Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mofanana ndi mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,Chikondi chokhulupirika chimene amasonyeza anthu amene amamuopa ndi chachikulu kwambiri.+
5 Inu Yehova, chikondi chanu chokhulupirika chafika kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika mpaka mʼmitambo.
11 Mofanana ndi mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,Chikondi chokhulupirika chimene amasonyeza anthu amene amamuopa ndi chachikulu kwambiri.+