Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+ Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+ Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+