Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu. Ezekieli 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* nʼkufa chifukwa cha zochita zakezo, adzakhala kuti wafa chifukwa cha zoipa zake.
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu.
26 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* nʼkufa chifukwa cha zochita zakezo, adzakhala kuti wafa chifukwa cha zoipa zake.