Mateyu 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 anapatsa Yesu vinyo wosakaniza ndi zinthu zowawa zamadzimadzi kuti amwe,+ koma iye atalawa, anakana kumwa. Maliko 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kumeneko anayesa kumupatsa vinyo wosakaniza ndi mule,+ koma iye anakana.
34 anapatsa Yesu vinyo wosakaniza ndi zinthu zowawa zamadzimadzi kuti amwe,+ koma iye atalawa, anakana kumwa.