Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu ananena kuti: “Popeza amandikonda,* ine ndidzamupulumutsa.+ Ndidzamuteteza chifukwa akudziwa* dzina langa.+ Yakobo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+
14 Mulungu ananena kuti: “Popeza amandikonda,* ine ndidzamupulumutsa.+ Ndidzamuteteza chifukwa akudziwa* dzina langa.+
12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+