Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+ Salimo 104:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndidzaimbira Yehova+ moyo wanga wonse.Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+
5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+
33 Ndidzaimbira Yehova+ moyo wanga wonse.Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+