15 Oimba, ana a Asafu,+ anali pa ntchito yawo mogwirizana ndi lamulo la Davide,+ la Asafu,+ la Hemani ndi la Yedutuni+ yemwe anali wamasomphenya wa mfumu. Alonda apageti anali pamageti osiyanasiyana.+ Iwo sankafunika kusiya ntchito yawo chifukwa Alevi abale awo anawakonzera nyama yawo.