-
Danieli 4:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 “Nthawi imeneyi itatha,+ ine Nebukadinezara ndinayangʼana kumwamba ndipo nzeru zanga zinabwerera. Ndinatamanda Wamʼmwambamwamba ndipo amene adzakhalepo mpaka kalekale ndinamutamanda ndi kumulemekeza, chifukwa ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo ufumu wake udzakhalapo kumibadwomibadwo.+
-