Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola nʼkukaima pathanthwe ku Horebe. Kumeneko ukamenye thanthwelo ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwe.”+ Mose anachitadi zomwezo pamaso pa akulu a Isiraeli. Numeri 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mose atatero, anakweza dzanja lake nʼkumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Ndiyeno madzi ambiri anayamba kutuluka ndipo gulu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+ Salimo 105:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anatsegula thanthwe ndipo panatuluka madzi ambiri.+Madziwo anayenda ngati mtsinje kudutsa mʼchipululu.+ Yesaya 48:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo sanamve ludzu pamene iye ankawatsogolera kudutsa mʼchipululu.+ Iye anachititsa kuti madzi atuluke pathanthwe kuti iwo amwe.Anangʼamba thanthwe nʼkupangitsa kuti madzi atuluke.”+ 1 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo onse ankamwa madzi auzimu ofanana.+ Chifukwa ankamwa pathanthwe lauzimu limene linkawatsatira, ndipo thanthwelo linali* Khristu.+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola nʼkukaima pathanthwe ku Horebe. Kumeneko ukamenye thanthwelo ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwe.”+ Mose anachitadi zomwezo pamaso pa akulu a Isiraeli.
11 Mose atatero, anakweza dzanja lake nʼkumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Ndiyeno madzi ambiri anayamba kutuluka ndipo gulu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+
41 Anatsegula thanthwe ndipo panatuluka madzi ambiri.+Madziwo anayenda ngati mtsinje kudutsa mʼchipululu.+
21 Iwo sanamve ludzu pamene iye ankawatsogolera kudutsa mʼchipululu.+ Iye anachititsa kuti madzi atuluke pathanthwe kuti iwo amwe.Anangʼamba thanthwe nʼkupangitsa kuti madzi atuluke.”+
4 Ndipo onse ankamwa madzi auzimu ofanana.+ Chifukwa ankamwa pathanthwe lauzimu limene linkawatsatira, ndipo thanthwelo linali* Khristu.+