Ekisodo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mose ali mʼphirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Choncho anthuwo anasonkhana kwa Aroni nʼkumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.” Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni* atanenepa, anapandukira mbuye wake. Iwe wanenepa, wakula thupi, wakhuta mopitirira muyezo.+ Choncho iye anasiya Mulungu amene anamupanga,+Ndipo ananyoza Thanthwe la chipulumutso chake.
32 Mose ali mʼphirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Choncho anthuwo anasonkhana kwa Aroni nʼkumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.”
15 Yesuruni* atanenepa, anapandukira mbuye wake. Iwe wanenepa, wakula thupi, wakhuta mopitirira muyezo.+ Choncho iye anasiya Mulungu amene anamupanga,+Ndipo ananyoza Thanthwe la chipulumutso chake.